2 Mbiri 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira.+ N’chifukwa chake iye anawabweretsera tsoka lonseli.’”+ Yeremiya 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo adzanena kuti: “Anauchitira zimenezi chifukwa chakuti anthu a mumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo+ ndi kuyamba kulambira milungu ina ndi kuitumikira.”’+
22 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira.+ N’chifukwa chake iye anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
9 Ndipo adzanena kuti: “Anauchitira zimenezi chifukwa chakuti anthu a mumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo+ ndi kuyamba kulambira milungu ina ndi kuitumikira.”’+