Levitiko 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+ Deuteronomo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+ N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka. Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+
25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+
30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+ N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+