Levitiko 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 pamenepo, ineyo ndidzatsutsana nanu,+ ndipo ndidzakukanthani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+ Ezekieli 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho ndinawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu, moti anamwazikira m’mayiko osiyanasiyana.+ Ndinawaweruza mogwirizana ndi njira zawo komanso zochita zawo.+
24 pamenepo, ineyo ndidzatsutsana nanu,+ ndipo ndidzakukanthani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+
19 Choncho ndinawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu, moti anamwazikira m’mayiko osiyanasiyana.+ Ndinawaweruza mogwirizana ndi njira zawo komanso zochita zawo.+