Yesaya 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+ Anthu adzakutchani atumiki+ a Mulungu wathu.+ Mudzadya zinthu zochokera ku mitundu ya anthu+ ndiponso mudzalankhula za inuyo mokondwera, chifukwa cha chuma ndi ulemerero zimene mudzapeze kwa mitunduyo.+ Yeremiya 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ponena za ansembe achilevi, pakati pawo sindidzasowa mwamuna wopereka nsembe zopsereza zathunthu, nsembe yambewu yofukiza komanso nsembe zina nthawi zonse.’”+ 1 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+
6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+ Anthu adzakutchani atumiki+ a Mulungu wathu.+ Mudzadya zinthu zochokera ku mitundu ya anthu+ ndiponso mudzalankhula za inuyo mokondwera, chifukwa cha chuma ndi ulemerero zimene mudzapeze kwa mitunduyo.+
18 Ndipo ponena za ansembe achilevi, pakati pawo sindidzasowa mwamuna wopereka nsembe zopsereza zathunthu, nsembe yambewu yofukiza komanso nsembe zina nthawi zonse.’”+
5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+