Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 42:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano utenge ng’ombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.+ Upite nazo kwa mtumiki wanga Yobu,+ ndipo inuyo mukadziperekere nsembe yopsereza. Ndiyeno Yobu mtumiki wanga akakupemphererani.+ Ine ndimvera iye yekhayo basi kuti ndisakuchititseni manyazi chifukwa cha zopusa zimene mwachita, popeza simunanene zoona za ine monga wachitira Yobu mtumiki wanga.”+

  • Ezekieli 20:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 “‘Nyumba yonse ya Isiraeli idzanditumikira m’phiri langa loyera,+ phiri lalitali la m’dziko la Isiraeli,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Kumeneko ndidzasangalala nawo ndipo ndidzafuna zopereka zanu ndi nsembe zanu za zinthu zoyambirira kucha pa zinthu zanu zonse zopatulika.+

  • Aroma 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu abale, kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe+ yamoyo,+ yoyera+ ndi yovomerezeka kwa Mulungu,+ ndiyo utumiki wopatulika+ mwa kugwiritsa ntchito luntha la kuganiza.+

  • 1 Petulo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena