Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo analitu kumupandukira kawirikawiri m’chipululu,+Anali kumukhumudwitsa m’chipululumo!+ Yesaya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero mneneriyo anati: “Tamverani inu a nyumba ya Davide. Kodi mukuona ngati n’zazing’ono kuti muzitopetsa anthu, ndiponso kuti mutopetse Mulungu wanga?+ Yesaya 63:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+
13 Chotero mneneriyo anati: “Tamverani inu a nyumba ya Davide. Kodi mukuona ngati n’zazing’ono kuti muzitopetsa anthu, ndiponso kuti mutopetse Mulungu wanga?+
10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+