Levitiko 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aroni ndi ana ake kuti asayandikire zinthu zopatulika za ana a Isiraeli ndi kuipitsa dzina langa loyera.+ Asayandikire zinthu zimene azipatula kuti azipereke nsembe kwa ine.+ Ine ndine Yehova. Numeri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azitumikira inuyo ndi kugwira ntchito zawo za pachihema chonse.+ Koma asamayandikire zipangizo za m’malo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo mungafe.+ Machitidwe 7:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 inu amene munalandira Chilamulo kudzera mwa angelo,+ koma osachisunga.”
2 “Uza Aroni ndi ana ake kuti asayandikire zinthu zopatulika za ana a Isiraeli ndi kuipitsa dzina langa loyera.+ Asayandikire zinthu zimene azipatula kuti azipereke nsembe kwa ine.+ Ine ndine Yehova.
3 Azitumikira inuyo ndi kugwira ntchito zawo za pachihema chonse.+ Koma asamayandikire zipangizo za m’malo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo mungafe.+