Numeri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azichita utumiki umene mwawapatsa komanso azigwira ntchito zawo zonse zapachihema.+ Koma asamayandikire zipangizo zamʼmalo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo musafe.+
3 Azichita utumiki umene mwawapatsa komanso azigwira ntchito zawo zonse zapachihema.+ Koma asamayandikire zipangizo zamʼmalo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo musafe.+