Ekisodo 30:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndipo uziyeretse kuti zikhale zoyera koposa.+ Aliyense wogwira zinthu zimenezi azikhala woyera.+ Levitiko 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Chilichonse chimene chingakhudze mnofu wake chidzakhala choyera,+ ndipo ngati munthu wadonthezera ena mwa magazi a nyamayo pachovala,+ chovala chimene wadonthezera magazicho muzichichapira kumalo oyera.+
27 “‘Chilichonse chimene chingakhudze mnofu wake chidzakhala choyera,+ ndipo ngati munthu wadonthezera ena mwa magazi a nyamayo pachovala,+ chovala chimene wadonthezera magazicho muzichichapira kumalo oyera.+