Levitiko 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe asakwatire hule+ kapena mkazi amene wataya unamwali wake. Asakwatirenso+ mkazi amene mwamuna wake anamusiya ukwati,+ chifukwa wansembeyo ndi woyera kwa Mulungu wake.
7 Wansembe asakwatire hule+ kapena mkazi amene wataya unamwali wake. Asakwatirenso+ mkazi amene mwamuna wake anamusiya ukwati,+ chifukwa wansembeyo ndi woyera kwa Mulungu wake.