Numeri 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu woteroyo azidziyeretsa ndi madzi oyeretsera aja pa tsiku lachitatu,+ ndipo pa tsiku la 7 azikhala woyera. Koma akapanda kudziyeretsa pa tsiku lachitatu, sadzakhala woyera pa tsiku la 7.
12 Munthu woteroyo azidziyeretsa ndi madzi oyeretsera aja pa tsiku lachitatu,+ ndipo pa tsiku la 7 azikhala woyera. Koma akapanda kudziyeretsa pa tsiku lachitatu, sadzakhala woyera pa tsiku la 7.