-
Ezekieli 40:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kenako ananditengera m’bwalo lamkati kudzera mbali ya kum’mawa. Kumeneko iye anayeza kanyumba ka pachipatako ndipo miyezo yake inali yofanana ndi tinyumba tina tija.
-