Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. 1 Mafumu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero mfumu inapita ku Gibeoni+ kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko ndiye kunali malo okwezeka ofunika kwambiri.+ Kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
4 Chotero mfumu inapita ku Gibeoni+ kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko ndiye kunali malo okwezeka ofunika kwambiri.+ Kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+