Ekisodo 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Kenako utenge nkhosa yowalongera unsembe ndi kuwiritsa nyama yake m’malo oyera.+ 2 Mbiri 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anaphika+ nsembe ya pasika+ pamoto malinga ndi mwambo wawo ndipo zinthu zopatulika anaziphika+ m’miphika, m’miphika ya pansi pozungulira ndi m’miphika yosalowa kwambiri. Atatero anapititsa nyamayo msangamsanga kwa ana onse a anthuwo.+
13 Kenako anaphika+ nsembe ya pasika+ pamoto malinga ndi mwambo wawo ndipo zinthu zopatulika anaziphika+ m’miphika, m’miphika ya pansi pozungulira ndi m’miphika yosalowa kwambiri. Atatero anapititsa nyamayo msangamsanga kwa ana onse a anthuwo.+