Genesis 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi m’bale wanga ndipo ndapambananso.” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+ Yoswa 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Maere a 6+ anagwera ana a Nafitali+ potsata mabanja awo.
8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi m’bale wanga ndipo ndapambananso.” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+