-
Ezekieli 48:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Miyezo ya mzindawo ikhale motere: Mbali ya kumpoto, mzindawo ukhale wautali mikono 4,500. Mbali ya kum’mwera ukhale wautali mikono 4,500. Mbali ya kum’mawa ukhale wautali mikono 4,500, ndipo mbali ya kumadzulo ukhalenso mikono 4,500.
-