Deuteronomo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehova adzakuyendetsa+ pamodzi ndi mfumu+ yako imene udzadziikira, kukupititsa ku mtundu umene iweyo kapena makolo ako simunaudziwe. Kumeneko udzatumikira milungu ina, yamtengo kapena yamwala.+ Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+ Yeremiya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+
36 Yehova adzakuyendetsa+ pamodzi ndi mfumu+ yako imene udzadziikira, kukupititsa ku mtundu umene iweyo kapena makolo ako simunaudziwe. Kumeneko udzatumikira milungu ina, yamtengo kapena yamwala.+
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+ Yeremiya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+
6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+