Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena: “Ine ndithana nawe mzinda iwe,+ ndipo ndidzapereka zigamulo pakati pako pamaso pa mitundu ya anthu.+

  • Ezekieli 16:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Iwo adzatentha nyumba zako ndi moto+ ndipo adzakulanga pamaso pa akazi ambiri.+ Ine ndidzakusiyitsa uhule+ moti sudzaperekanso malipiro.

  • Yuda 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kudzapereka chiweruzo kwa onse,+ ndi kudzagamula kuti onse osaopa Mulungu apezeka ndi mlandu chifukwa cha ntchito zawo zonyoza Mulungu zimene anazichita mosaopa Mulungu, komanso chifukwa cha zinthu zonse zonyoza koopsa zimene ochimwa osaopa Mulungu anamunenera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena