Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+

  • 2 Mafumu 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero wansembe Hilikiya, Ahikamu, Akibori, Safani, ndi Asaya anapita kukalankhula ndi Hulida mneneri wamkazi.+ Hulida anali mkazi wa Salumu yemwe anali wosamalira zovala, mwana wa Tikiva, mwana wa Harihasi,+ ndipo Hulidayo anali kukhala kumbali yatsopano ya mzinda wa Yerusalemu.+

  • Luka 2:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kunalinso Anna mneneri wamkazi, mwana wa Fanueli, wa fuko la Aseri. Mayi ameneyu anali wachikulire kwambiri, ndipo anakhala ndi mwamuna wake zaka 7 zokha kuchokera pa unamwali wake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena