Deuteronomo 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anayamba kuputa nsanje+ yake ndi milungu yachilendo.+Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi zinthu zonyansa.+ Yeremiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+
16 Anayamba kuputa nsanje+ yake ndi milungu yachilendo.+Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi zinthu zonyansa.+
5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi chiyani chosalungama+ kuti akhale patali ndi ine?+ Anandipeza ndi chiyani kuti ayambe kutsatira fano lopanda pake+ iwonso n’kukhala anthu opanda pake?+