Salimo 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzasamba m’manja mwanga kusonyeza kuti ndine wopanda cholakwa,+Ndipo ndidzayenda mozungulira guwa lanu lansembe, inu Yehova,+ Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+
6 Ndidzasamba m’manja mwanga kusonyeza kuti ndine wopanda cholakwa,+Ndipo ndidzayenda mozungulira guwa lanu lansembe, inu Yehova,+ Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+