-
Salimo 26:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndidzasamba m’manja mwanga kusonyeza kuti ndine wopanda cholakwa,+
Ndipo ndidzayenda mozungulira guwa lanu lansembe, inu Yehova,+
-