Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Yesaya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wati: “Ana aakazi a Ziyoni ndi odzikuza. Iwo amayenda atasolola makosi awo ndiponso amakopa amuna ndi maso awo. Amayenda modzigomera, ndipo akamayenda mapazi awo amachita phokoso chifukwa cha zokongoletsera zimene amavala m’mapazi.+ Yeremiya 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Tamverani anthu inu. Tcherani khutu. Musadzikweze+ pakuti Yehova ndi amene wanena zimenezi.+ 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
16 Yehova wati: “Ana aakazi a Ziyoni ndi odzikuza. Iwo amayenda atasolola makosi awo ndiponso amakopa amuna ndi maso awo. Amayenda modzigomera, ndipo akamayenda mapazi awo amachita phokoso chifukwa cha zokongoletsera zimene amavala m’mapazi.+
5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+