Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni, chilango chimene anakupatsa chifukwa cha zolakwa zako chatha.+ Sadzakutenganso kupita nawe ku ukapolo.+

      Tsopano iwe mwana wamkazi wa Edomu, Mulungu watembenukira kwa iwe kuti aone zolakwa zako. Machimo ako wawaika poyera.+

  • Ezekieli 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Anthu inu, adani anu adzakugwirani chifukwa chakuti zolakwa zanu zinaululidwa ndipo munachititsa kuti zikumbukiridwe.+ Ndithu adzakugwirani chifukwa machimo anu, kapena kuti zochita zanu zauchimo zinaonekera ndipo simunaiwalidwe.’+

  • Hoseya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ndidzamuvula kuti amuna omukonda kwambiriwo aone maliseche ake,+ ndipo palibe mwamuna amene adzamukwatula m’dzanja langa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena