Yeremiya 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kodi sunamve zimene ena mwa anthu awa akunena kuti, ‘Mabanja awiri amene Yehova wasankha,+ adzawakananso’? Adani akuchitira anthu anga zachipongwe+ ndipo sakuwaonanso ngati mtundu wa anthu.
24 “Kodi sunamve zimene ena mwa anthu awa akunena kuti, ‘Mabanja awiri amene Yehova wasankha,+ adzawakananso’? Adani akuchitira anthu anga zachipongwe+ ndipo sakuwaonanso ngati mtundu wa anthu.