Maliro 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Makolo athu ndi amene anachimwa.+ Iwo anafa, koma ifeyo ndi amene tikuvutika ndi zolakwa zawozo.+ Ezekieli 23:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anthu amenewo adzakulangani chifukwa cha khalidwe lanu lotayirira+ komanso mudzalangidwa chifukwa cha machimo amene munachita ndi mafano anu onyansa. Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+
49 Anthu amenewo adzakulangani chifukwa cha khalidwe lanu lotayirira+ komanso mudzalangidwa chifukwa cha machimo amene munachita ndi mafano anu onyansa. Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+