Yeremiya 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya,+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anamuika kukhala mfumu m’dziko la Yuda,+ anayamba kulamulira m’malo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu.+ Ezekieli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera apo, inatenga mmodzi wa mbewu yachifumu+ n’kuchita naye pangano ndi kumulumbiritsa.+ Mfumuyo inatenga atsogoleri a m’dzikolo n’kupita nawo kwawo,+
37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya,+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anamuika kukhala mfumu m’dziko la Yuda,+ anayamba kulamulira m’malo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu.+
13 Kuwonjezera apo, inatenga mmodzi wa mbewu yachifumu+ n’kuchita naye pangano ndi kumulumbiritsa.+ Mfumuyo inatenga atsogoleri a m’dzikolo n’kupita nawo kwawo,+