Deuteronomo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+ 1 Samueli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+Wotsitsa ndiponso Wokweza,+
43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+