Salimo 81:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaika chigamulocho monga chikumbutso kwa Yosefe,+Pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo.+Ndinali kumva chilankhulo chimene sindinali kuchidziwa.+ Yesaya 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Simudzaona anthu achipongwe, amene chilankhulo chawo n’chovuta kumva, anthu achibwibwi olankhula zinthu zovuta kumva.+
5 Anaika chigamulocho monga chikumbutso kwa Yosefe,+Pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo.+Ndinali kumva chilankhulo chimene sindinali kuchidziwa.+
19 Simudzaona anthu achipongwe, amene chilankhulo chawo n’chovuta kumva, anthu achibwibwi olankhula zinthu zovuta kumva.+