Ekisodo 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Farao atalola kuti ana a Isiraeli apite, Mulungu sanawadutsitse m’dziko la Afilisiti ngakhale kuti kunali kufupi, pakuti Mulungu anati: “Anthu angataye mtima atakumana ndi nkhondo ndipo angabwerere ku Iguputo.”+ Ekisodo 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Mose anauza Isiraeli kuti anyamuke pa Nyanja Yofiira ndipo analowa m’chipululu cha Shura.+ Iwo anayenda m’chipululumo kwa masiku atatu, koma sanapeze madzi.+
17 Farao atalola kuti ana a Isiraeli apite, Mulungu sanawadutsitse m’dziko la Afilisiti ngakhale kuti kunali kufupi, pakuti Mulungu anati: “Anthu angataye mtima atakumana ndi nkhondo ndipo angabwerere ku Iguputo.”+
22 Kenako Mose anauza Isiraeli kuti anyamuke pa Nyanja Yofiira ndipo analowa m’chipululu cha Shura.+ Iwo anayenda m’chipululumo kwa masiku atatu, koma sanapeze madzi.+