Numeri 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+“Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+ Salimo 106:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,+Kuti adzawapha m’chipululu,+
30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+