Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Pambuyo pa zimenezi, ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku*+ koma chinali ndi mapiko anayi a mbalame pamsana pake. Chilombochi chinali ndi mitu inayi+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro.

  • Danieli 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+

  • Danieli 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho iye anandiuza kuti:

      “Kodi ukudziwadi kuti n’chifukwa chiyani ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Pamene ndikupita, nayenso kalonga wa Girisi akubwera.+

  • Danieli 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ndiyeno mfumu yamphamvu idzauka ndi kulamulira ndi mphamvu zazikulu,+ ndipo idzachitadi zofuna zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena