Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ndiyeno ndinali ndi chidwi chofuna kudziwa zambiri zokhudza chilombo chachinayi chija, chimene chinali chosiyana ndi zina zonse. Chilombo chimenechi chinali choopsa kwambiri. Mano ake anali achitsulo, zikhadabo zake zinali zamkuwa, ndipo chinali kudya zinthu ndi kuziphwanyaphwanya. Zotsala chinali kuzipondaponda ndi mapazi ake.+

  • Danieli 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Ndiyeno iye anandiuza kuti, ‘Ponena za chilombo chachinayi chimenechi, pali ufumu wachinayi umene udzakhalapo padziko lapansi. Udzakhala wosiyana ndi maufumu ena onse. Udzadya dziko lonse lapansi ndipo udzalipondaponda ndi kuliphwanyaphwanya.+

  • Yohane 11:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ngati timulekerera, onse adzakhulupirira mwa iye,+ ndipo Aroma+ adzabwera kudzatenga malo athu+ ndi mtundu wathu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena