Danieli 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 miyendo yake inali yachitsulo,+ ndipo mapazi ake anali achitsulo chosakanizika ndi dongo.+