1 Mafumu 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chakudya cha kunyumba yachifumu ya Solomo tsiku lililonse chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,*+ ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori, Danieli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku 10 amenewo atatha, iwo anali kuoneka bwino kwambiri ndiponso matupi awo ankaoneka athanzi kuposa ana onse amene anali kudya zakudya zabwino za mfumu.+
22 Chakudya cha kunyumba yachifumu ya Solomo tsiku lililonse chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,*+ ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori,
15 Masiku 10 amenewo atatha, iwo anali kuoneka bwino kwambiri ndiponso matupi awo ankaoneka athanzi kuposa ana onse amene anali kudya zakudya zabwino za mfumu.+