Danieli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma mukandiuza malotowo ndi kuwamasulira, ine ndikupatsani mphatso, mphoto ndi ulemerero wochuluka.+ Choncho ndiuzeni malotowo ndipo muwamasulire.” Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+
6 Koma mukandiuza malotowo ndi kuwamasulira, ine ndikupatsani mphatso, mphoto ndi ulemerero wochuluka.+ Choncho ndiuzeni malotowo ndipo muwamasulire.”
29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+