Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo.

  • Danieli 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno mfumuyo inafuula kuti aibweretsere olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi okhulupirira nyenyezi.+ Mfumuyo inauza amuna anzeru a m’Babulo amenewa kuti: “Aliyense amene angawerenge mawuwa ndi kundiuza kumasulira kwake, ndimuveka zovala zofiirira*+ ndi mkanda wagolide m’khosi, ndipo ndimuika kukhala wolamulira wachitatu mu ufumuwu.”+

  • Danieli 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndamvanso kuti iweyo umatha kumasulira zinthu+ ndi kumasula mfundo. Tsopano ngati ungathe kuwerenga mawuwa ndi kundiuza kumasulira kwake, ndikuveka zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi, ndipo ndikuika kukhala wolamulira wachitatu mu ufumuwu.”+

  • Danieli 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena