Salimo 66:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Bwerani, mvetserani, inu nonse oopa Mulungu, ndipo ine ndifotokoza+Zimene wandichitira.+ Danieli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikukutamandani ndi kukuyamikani,+ inu Mulungu wa makolo anga, chifukwa mwandipatsa nzeru+ ndi mphamvu. Tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani, pakuti mwatidziwitsa zimene mfumu inali kufuna.”+
23 Ndikukutamandani ndi kukuyamikani,+ inu Mulungu wa makolo anga, chifukwa mwandipatsa nzeru+ ndi mphamvu. Tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani, pakuti mwatidziwitsa zimene mfumu inali kufuna.”+