Salimo 145:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Ndipo ukulu wake ndi wosasanthulika.+ Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:
28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: