Levitiko 11:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 kuti muzisiyanitsa+ chodetsedwa ndi choyera komanso zamoyo zimene muyenera kudya ndi zimene simuyenera kudya.’” Salimo 119:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Odala ndi anthu amene amasunga zikumbutso zake,+Amene amayesetsa kumufunafuna ndi mtima wonse.+ Ezekieli 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anapitiriza kunena kuti: “Mofanana ndi zimenezi, ana a Isiraeli azidzadya chakudya chodetsedwa+ pakati pa mitundu yosiyanasiyana imene ndidzawathamangitsireko.”+
47 kuti muzisiyanitsa+ chodetsedwa ndi choyera komanso zamoyo zimene muyenera kudya ndi zimene simuyenera kudya.’”
13 Yehova anapitiriza kunena kuti: “Mofanana ndi zimenezi, ana a Isiraeli azidzadya chakudya chodetsedwa+ pakati pa mitundu yosiyanasiyana imene ndidzawathamangitsireko.”+