Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yehova amanyansidwa ndi munthu aliyense wa mtima wonyada.+ Ngakhale anthu atagwirana manja, munthu sangapewe chilango.+

  • Yesaya 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+

  • Danieli 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+

  • Mika 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena