Salimo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+
3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+