Mateyu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Odala ndi anthu amene ali ofatsa,+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+ Mateyu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+ Luka 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndikuchita nanu pangano,+ mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+
28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+