Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako anamupatsa ulamuliro,+ ulemerero,+ ndi ufumu+ kuti anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana azimutumikira.+ Ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo sudzatha. Ufumu wake sudzawonongedwa.+

  • Mateyu 20:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye anafunsa mayiyo kuti: “Mukufuna chiyani?” Mayiyo anati: “Lonjezani kuti ana angawa adzakhala, mmodzi kudzanja lanu lamanja, wina kumanzere kwanu, mu ufumu wanu.”+

  • Mateyu 25:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+

  • Luka 18:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Palibe amene wasiya nyumba, mkazi, abale, makolo kapena ana, chifukwa cha ufumu wa Mulungu+

  • Luka 22:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 kuti mukadye+ ndi kumwa patebulo langa mu ufumu wanga,+ ndipo mukakhala m’mipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.

  • 1 Akorinto 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kapena simukudziwa kuti oyerawo adzaweruza+ dziko?+ Ndipo ngati mudzaweruza dziko, kodi simungathe kuzenga milandu yaing’ono kwambiri+ ngati imeneyo?

  • Chivumbulutso 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako ndinaona mipando yachifumu+ ndi amene anakhalapo. Iwo anapatsidwa mphamvu yoweruza.+ Ndiyeno ndinaona miyoyo ya amene anaphedwa ndi nkhwangwa chifukwa cha kuchitira umboni za Yesu, ndi kulankhula za Mulungu. Ndinaonanso anthu amene sanalambire chilombo+ kapena chifaniziro chake,+ ndipo sanalandire chizindikiro pamphumi pawo ndi padzanja pawo.+ Iwo anakhalanso ndi moyo ndipo analamulira monga mafumu+ limodzi ndi Khristu zaka 1,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena