Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “‘Chifukwa chakuti inu mfumu munaona mlonda woyera+ akutsika kuchokera kumwamba, akunena kuti: “Gwetsani mtengowo ndipo muuwononge, koma musiye chitsa chake munthaka, mutachikulunga ndi mkombero wachitsulo ndi wamkuwa, chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba, chikhale limodzi ndi nyama zakutchire kufikira patadutsa nthawi zokwanira 7,”+

  • Luka 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena