Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno inu mfumu munaona mlonda,+ mthenga woyera akutsika kuchokera kumwamba, ndipo ankanena kuti: “Gwetsani mtengowo ndipo muuwononge, koma musiye chitsa ndi mizu yake munthaka ndipo muchikulunge ndi mkombero wachitsulo ndi wakopa.* Chitsacho chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba. Chizikhala limodzi ndi nyama zakutchire mpaka patadutsa nthawi zokwana 7.”+

  • Danieli
    Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019
    • 4:23

      Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32

      Ulosi wa Danieli, ptsa. 94-97

      Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 140-141

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena