Danieli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo. Danieli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Tsopano ineyo Danieli, ndinavutika kwambiri mumtima chifukwa cha zimenezi ndipo ndinachita mantha ndi masomphenya amene ndinaona.+
7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo.
15 “Tsopano ineyo Danieli, ndinavutika kwambiri mumtima chifukwa cha zimenezi ndipo ndinachita mantha ndi masomphenya amene ndinaona.+