Danieli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼchaka choyamba cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara+ ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Ndiyeno analemba zimene analotazo+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 129 Nsanja ya Olonda,10/1/1986, ptsa. 4, 6
7 Mʼchaka choyamba cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara+ ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Ndiyeno analemba zimene analotazo+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo.