Danieli 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+ Luka 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe. Luka 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’mwezi wake wa 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa Galileya, wotchedwa Nazareti.
21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+
19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe.
26 M’mwezi wake wa 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa Galileya, wotchedwa Nazareti.