Danieli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu a munthu wochokera kufumbi ali pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anafuula kuti: “Gabirieli,+ thandiza uyo ali apoyo kuti amvetsetse zimene waona.”+ Luka 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe.
16 Kenako ndinamva mawu a munthu wochokera kufumbi ali pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anafuula kuti: “Gabirieli,+ thandiza uyo ali apoyo kuti amvetsetse zimene waona.”+
19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe.